Zowonedwa ndi ambiri

Chithandizo kwa ife

Yazid ayenera kutembeleredwa mpaka tsiku la Qiyama.


Yazid ayenera kutembeleredwa mpaka tsiku la Qiyama.

( 0 Votes ) 

Yazid ayenera kutembeleredwa mpaka tsiku la Qiyama.
 

grey Yazid ayenera kutembeleredwa mpaka tsiku la Qiyama.

Munthu wina mdziko la Saud Arabia yemwe ndi olalikira kwa anthu wanena kuti Yazid mwana wa Muawiyah ayenera kutembeleredwa mpaka tsiku lachimaliziro.
Mkuluyu yemwe amadziwika ndi dzina loti Sa’ad  Duraihim adalemba mu news pepala ina  yotchedwa Al-mursad kuti Yazid mwana wa Muawiyah yemwe adali mtsogoleri wa mtundu wa Umayyah  ayenera kutembeleredwa chifukwa cha ntchito yoipa ndi yonyasa yomwe adachita kwa anthu amzinda wa Madinah.
Koma kulankhula kwa mkuluyu kwatsatizidwa ndi kutsutsa kuchokera kwa anthu osiyana siyana chifukwa choti anthu ambiri amalemekeza atsogoleri ama Umayyah kwambiri ndipo sakondwa ndikuti munthu wina atchule zoipa zawo.
Angakhale zili choncho zoona zake ndizoti zomwe mkuluyu wanena ndizoona chifukwa choti  zidachitika mu history ya chisilamu kuti Yazid mwana wa Muawiyah adapha anthu ambiri osalakwa  omwe ambiri awo adali ma swahaba kapena ana maswahaba aMtumiki (s.a.w.).  

Kuwonjezera ganizogrey Yazid ayenera kutembeleredwa mpaka tsiku la Qiyama.
zikhale zatsopano


sharethis Yazid ayenera kutembeleredwa mpaka tsiku la Qiyama.

Kutumiza funso

ایمیل شما منتشر نمی شود.
Malo okakamizidwa kudzadzitsamo akudziwika ndi chizindikiro ichi * .

*


2 × = چهار

Kulumikizana ndi ife | RSS |Zolinga za Site

Ufulu onse wa Site yofalitsa uthenga ya Islam 14 ndi otetezedwa ndipo zikuloledwa kugwiritsa ntchito zinthuzi potchula komwe zachokera.