Zowonedwa ndi ambiri

Chithandizo kwa ife

Zolankhula za Imam Ali (a.s)5.


Zolankhula za Imam Ali (a.s)5.

( 0 Votes ) 

Zolankhula za Imam Ali (a.s)5.
Imam Ali (a.s) adati:
جهل المرء بعُیُوبه من أکبر ذنوبه.
-Kusadziwa kwa munthu zolakwa ndi zoipa zake kuli  koipa kuposa machimo ake.
- Chifukwa munthu akadziwa kulakwa ndikuipa kwake atha kusintha ndikukhala munthu ogwira ntchito zabwino komanso mwina atha kubwelera mwa Mulungu.
-Munthu yemwe sangadziwe zoipa zake ndiye kuti alibe chiyembekezo chosintha komanso kubwelera mwa Mulungu.
 

Kuwonjezera ganizogrey Zolankhula za Imam Ali (a.s)5.
zikhale zatsopano


sharethis Zolankhula za Imam Ali (a.s)5.

Kutumiza funso

ایمیل شما منتشر نمی شود.
Malo okakamizidwa kudzadzitsamo akudziwika ndi chizindikiro ichi * .

*


یک × 2 =

Kulumikizana ndi ife | RSS |Zolinga za Site

Ufulu onse wa Site yofalitsa uthenga ya Islam 14 ndi otetezedwa ndipo zikuloledwa kugwiritsa ntchito zinthuzi potchula komwe zachokera.