Zowonedwa ndi ambiri

Chithandizo kwa ife

Kupha ku Gaza


Kupha ku Gaza

( 0 Votes ) 

Kupha ku Gaza
 

grey Kupha ku Gaza
Nkhani yodandaulitsa ndiyoti maiko ena achiluya mmalo mothandiza Gaza akukhala limodzi ndi dziko loipisitsa kwambiri la Israel lomwe likupha anthu osalakwa kwambirinso ana ndi akazi.
Dziko la Egypt komanso Saud  ndi omwe akuthandiza Israel.
Manews pepala osiyana siyana  alengezetsa kuti atolankhani osiyana siyana adziko la Palestine komanso Egypt ndi Saud  aikira umboni ndi kuvomereza nkhaniyi zinthu zomwe zili zomvetsa chisoni kwambiri kwa asilamu onse dziko lapansi. Tsono ngati asilamu sitikuthandiza Gaza  ndindani yemwe angathandize???….

Kuwonjezera ganizogrey Kupha ku Gaza
zikhale zatsopano


sharethis Kupha ku Gaza

Kutumiza funso

ایمیل شما منتشر نمی شود.
Malo okakamizidwa kudzadzitsamo akudziwika ndi chizindikiro ichi * .

*


2 × = دو

Kulumikizana ndi ife | RSS |Zolinga za Site

Ufulu onse wa Site yofalitsa uthenga ya Islam 14 ndi otetezedwa ndipo zikuloledwa kugwiritsa ntchito zinthuzi potchula komwe zachokera.