Zowonedwa ndi ambiri

Chithandizo kwa ife

Saud ipereka ndalama kwa anthu


Saud ipereka ndalama kwa anthu

( 0 Votes ) 

Saud ipereka ndalama kwa anthu.

grey Saud ipereka ndalama kwa anthu
 
Dziko la Saud Arabia pakumva kuti anthu ena akufuna kwabwino azipereka kufuna kulowa gulu lankhondo la Iraq polimbana ndi Isil, lidapereka ndalama zokwana 1500 dollars kwa anthu okwana makumi anayi aliyense powanyengerera kuti   asapite kukamenya nkhondo ndi gulu la Isil.
Powonjezera ndalamazi adaperekanso magalimoto abwino kwa anthu ena.
Dziko la Saud lidagwirizana ndi gulu la Isil zoti akapeza zitsime za mafuta ku Iraq awagula.

Kuwonjezera ganizogrey Saud ipereka ndalama kwa anthu
zikhale zatsopano


sharethis Saud ipereka ndalama kwa anthu

Kutumiza funso

ایمیل شما منتشر نمی شود.
Malo okakamizidwa kudzadzitsamo akudziwika ndi chizindikiro ichi * .

*


− یک = 4

Kulumikizana ndi ife | RSS |Zolinga za Site

Ufulu onse wa Site yofalitsa uthenga ya Islam 14 ndi otetezedwa ndipo zikuloledwa kugwiritsa ntchito zinthuzi potchula komwe zachokera.