Zowonedwa ndi ambiri

Chithandizo kwa ife

Kupulumutsa nzinda wa Sanjar.


Kupulumutsa nzinda wa Sanjar.

( 0 Votes ) 

grey Kupulumutsa nzinda wa Sanjar.
 
Asilikali aboma la Iraq akwanitsa kupulumutsa nzinda wa Sanjar komanso malo a Humah kuchokera mmanja mwa  gulu lowukira la Isil. Gululi lidalanda malowa loweruka lapita kenako lolemba asilikali aboma adalowa munzindawu ndikuyamba kulimbana ndi gululi mpaka adaligonjetsa ndipo mukulankhula kwa wamkulu wa asilikaliwa adanena kuti  anthu ambiri agulu la Isil adaphedwa ndipo ena adavulala mukumenyanaku.
Pofuna kuthandiza asilikaliwa Nuri Malikiy adalamula kuti ndege yankhondo ipite ndikukathandiza komwe adaphanso anthu ambiri agululi malo monga Al-baaj ndi ena.
 
grey Kupulumutsa nzinda wa Sanjar.

Kuwonjezera ganizogrey Kupulumutsa nzinda wa Sanjar.
zikhale zatsopano


sharethis Kupulumutsa nzinda wa Sanjar.

Kutumiza funso

ایمیل شما منتشر نمی شود.
Malo okakamizidwa kudzadzitsamo akudziwika ndi chizindikiro ichi * .

*


+ دو = 4

Kulumikizana ndi ife | RSS |Zolinga za Site

Ufulu onse wa Site yofalitsa uthenga ya Islam 14 ndi otetezedwa ndipo zikuloledwa kugwiritsa ntchito zinthuzi potchula komwe zachokera.