Zowonedwa ndi ambiri

Chithandizo kwa ife

Hule ndi Wamkulu wa Gulu lowukira la Isil.


Hule ndi Wamkulu wa Gulu lowukira la Isil.

( 0 Votes ) 

grey Hule ndi Wamkulu wa Gulu lowukira la Isil.
 
News pepala  ina yotchedwa Annahar yaku Egypt yalemba nkhani yoti mkazi wina yemwe ndi odziwika popanga zinthu zosalongosoka (uhule) wadziko la Egypt ndi okondeka wa Abubakar Al-baghdadi amene amazitcha kuti ndi mtsogoleri wa gulu lowukira la Isil, zomwe zikusonyeza kutaika kwa mkuluyu ndikuipa kwa chikhalidwe chake. Msilamu lero lino ayenera kuchenjera ndi anthu ngati amenewa osamangomvera wina aliyense pazochitika, chikakhala chiphunzitso cha chisilamu ndichodziwika  bwino m’bale wanga iwe ukuwerenga nkhaniyi. Choncho samala, chifukwa  satana amabwera ndizokoma zake, monga munthu ofuna kukalowa kumtendere akumuitanira kuti azikapha anthu osalakwa akafuna mkazi azikatenga mahule akatero yawo ndi jannah, chisilamu chake chakuti chikuphunzitsa zimenezo, munthu wanzeru owopa Mulungu sangatengeke ndi bodza ngati limeneli koma yekhayo otsatira zofuna zamtima wake ndiye amene akumvera zimenezo.

Kuwonjezera ganizogrey Hule ndi Wamkulu wa Gulu lowukira la Isil.
zikhale zatsopano


sharethis Hule ndi Wamkulu wa Gulu lowukira la Isil.

Kutumiza funso

ایمیل شما منتشر نمی شود.
Malo okakamizidwa kudzadzitsamo akudziwika ndi chizindikiro ichi * .

*


− یک = 5

Kulumikizana ndi ife | RSS |Zolinga za Site

Ufulu onse wa Site yofalitsa uthenga ya Islam 14 ndi otetezedwa ndipo zikuloledwa kugwiritsa ntchito zinthuzi potchula komwe zachokera.