Zowonedwa ndi ambiri

Chithandizo kwa ife

Gaza.


Gaza.

( 0 Votes ) 

grey Gaza.
 
Ichi ndi chimodzi mwa zithunzi zomwe zili zomvetsa chisoni kwambiri  zomwe zikuwonetsera mmene Israel ikuphera ana osalakwa ku Gaza mudziko la Palestine.
Ndithudi tikakhala ife Asilamu kulankhula kwathu tikuti:
(( بأی ذنب قتلت))
Kodi ana amenewa akuphedweranji???
Ana amenewa adaphedwa  ndi mabomba omwe asilikali a Israel adaphulitsa mdera lawo ndipo iwo atawona kuti zamoyo palibe adangogwirana kuti m’bale wanga limba mtima tiye kwa Mulungu komwe tikasimbe za imfa yathu titagwirana chonchi, inde ndiwe m’bale wanga……….

Kuwonjezera ganizogrey Gaza.
zikhale zatsopano


sharethis Gaza.

Kutumiza funso

ایمیل شما منتشر نمی شود.
Malo okakamizidwa kudzadzitsamo akudziwika ndi chizindikiro ichi * .

*


هشت × 5 =

Kulumikizana ndi ife | RSS |Zolinga za Site

Ufulu onse wa Site yofalitsa uthenga ya Islam 14 ndi otetezedwa ndipo zikuloledwa kugwiritsa ntchito zinthuzi potchula komwe zachokera.