Zowonedwa ndi ambiri

Chithandizo kwa ife

Ndife okhonzeka.


Ndife okhonzeka.

( 0 Votes ) 

grey Ndife okhonzeka.
 
Wamkulu wa asilikali mdziko la  Iran  wanena kuti gulu lake ndilokonzeka kuthidzimula Israel  chifukwa chakhanza zomwe akuchita ku Gaza pomangopha anthu osalakwa kwakukulu kwake ana ndi akazi opanda mphamvu. Mkuluyu polankhula mau akewa adapitiliza kunena kuti gulu lake lankhondo ndilokhonzeka kuchotsa Israel pa map chifukwa iyi ndi ntchito yawo pofuna kuteteza anthu ofowoka komanso asilamu oponderezedwa.
Mkuluyu yemwe  ndi Muhammad Ali Jafari adalankhula mauwa pomwe adali pamsonkhano okambirana zamomwe nkhondo ikuyendera ku Gaza.
Iye adanena  kuti: “Ife pofuna kuthandiza sitiyang’ana kuti uyu ndi msilamu wa gulu liti ayi kuti kodi ndi wa Sunni kapena wa Shia, koma tithandiza mosayang’ana nkhope chifukwa ndiudindo wathu kutero.”  

Kuwonjezera ganizogrey Ndife okhonzeka.
zikhale zatsopano


sharethis Ndife okhonzeka.

Kutumiza funso

ایمیل شما منتشر نمی شود.
Malo okakamizidwa kudzadzitsamo akudziwika ndi chizindikiro ichi * .

*


+ 9 = سیزده

Kulumikizana ndi ife | RSS |Zolinga za Site

Ufulu onse wa Site yofalitsa uthenga ya Islam 14 ndi otetezedwa ndipo zikuloledwa kugwiritsa ntchito zinthuzi potchula komwe zachokera.