Zowonedwa ndi ambiri

Chithandizo kwa ife

Mizikiti yaku Europe.


Mizikiti yaku Europe.

( 0 Votes ) 

grey Mizikiti yaku Europe.
 
Mizikiti yaku Europe yomwe  idamangidwa ndi dziko la Saud Arabia ndi malo omwe chikuchokera chiwembu ndi gulu la ma wahabi.
Mkulu wina olongosola nkhani waku Europe wanena kuti dziko la Saud Arabia ndi dziko lomwe lili ndi mafuta ambiri komanso kochokera ziwembu ndi ma wahabi komanso maganizo opsola muyezo.
Mkuluyu yemwe ndi David Graner popitiliza kulankhula kwake adati: “Dziko la Saud Arabia ndi dziko lomwe likutuma magulu owukira ambiri pomanamizira dzina la Jihad ndikuwaphunzitsa ziphunzitso zosakhala bwino zomwe mapeto ake ndikupha anthu osalakwa. Saud Arabia kuyambira mchaka cha 1990, idayamba  ntchito yomanga mizikiti madera osiyana siyana ku Europe monga Bosnia, Macedonia ndi ena ndicholinga chofuna kupititsa patsogolo zikhulupiriro za chiwahabi, ndichifukwa chake tikuwona lero lino kuti magulu owukira ali ndizikhulupiriro zachiwahabi monga Isil. Ndichifukwa chakenso zochitika za gulu la Isil ndi kuwononga malo ena alionse omwe akuwona kuti asilamu amabwerapo kudzapanga ziyara (kuyenderapo kudzawona) ntchito yomwe gulu la mawahabi adayiyamba zaka 200 zapita ndipo ndinkhani yodziwika kwa munthu ofufuza nkhani kuti dziko la Saud lidakhazikitsidwa ndi mawahabi.”

Kuwonjezera ganizogrey Mizikiti yaku Europe.
zikhale zatsopano


sharethis Mizikiti yaku Europe.

Kutumiza funso

ایمیل شما منتشر نمی شود.
Malo okakamizidwa kudzadzitsamo akudziwika ndi chizindikiro ichi * .

*


شش − = 2

Kulumikizana ndi ife | RSS |Zolinga za Site

Ufulu onse wa Site yofalitsa uthenga ya Islam 14 ndi otetezedwa ndipo zikuloledwa kugwiritsa ntchito zinthuzi potchula komwe zachokera.