Zowonedwa ndi ambiri

Chithandizo kwa ife

Gulu la Isil muzithunzi.


Gulu la Isil muzithunzi.

( 0 Votes ) 

Apa America ndi Saud ikutuma gulu la Isil kuti lizipha anthu koma onsewa cholinga chawo ndizolowa zawo.

 grey Gulu la Isil muzithunzi.
Apa gululi likugwira ntchito yopha anthu tsopano

grey Gulu la Isil muzithunzi.
 
Apa nthu ena agululi akuvala zovala zachikazi pofuna kuziteteza ndichilamulo cha wamkulu wa gululi.
 

grey Gulu la Isil muzithunzi.
Kugwirana chanza kwa mtundu wa Shimr ndi gulu la Isil.
 

grey Gulu la Isil muzithunzi.
Atsogoleri a Iraq akunena kuti dziko lawo lithana ndimavuto palokha.
 

grey Gulu la Isil muzithunzi.
Apa asilikali agululi akulengezetsa zoti pofuna kuti nzimu wa Shimr ukhale pamtendere ayenera kupha munthu wina aliyense yemwe angamuwona munsewo chifukwa kuyenda munsewo ndi koletsedwa.
 

grey Gulu la Isil muzithunzi.
Apa gululi lalengezetsa za ukwati wa jihad, zomwe zapangitsa kuti angakhale mahule omwe kukalowa nawo gululi.
Opanga zimenezi wake ndi mtendere. Kutanthauza kuti:
Chiwerewere=mtendere
Kusewera ndi chisilamu kupose apa???…
 
 grey Gulu la Isil muzithunzi.

grey Gulu la Isil muzithunzi.
Apa maguluwa adayamba kumenyana okha okha kenako wahabi akunena kuti sayenera kumenyana chifukwa akazi ndi ana aku Syria osatetezedwa  adakali mmanja mwawobe.
 
grey Gulu la Isil muzithunzi.

Kuwonjezera ganizogrey Gulu la Isil muzithunzi.
zikhale zatsopano


sharethis Gulu la Isil muzithunzi.

Kutumiza funso

ایمیل شما منتشر نمی شود.
Malo okakamizidwa kudzadzitsamo akudziwika ndi chizindikiro ichi * .

*


× شش = 42

Kulumikizana ndi ife | RSS |Zolinga za Site

Ufulu onse wa Site yofalitsa uthenga ya Islam 14 ndi otetezedwa ndipo zikuloledwa kugwiritsa ntchito zinthuzi potchula komwe zachokera.