Zowonedwa ndi ambiri

Chithandizo kwa ife

Malesyians ena agwida ndi mankhwala ozunguza ubongo.


Malesyians ena agwida ndi mankhwala ozunguza ubongo.

( 0 Votes ) 

Malesyians ena agwida ndi mankhwala ozunguza ubongo.
 

grey Malesyians ena agwida ndi mankhwala ozunguza ubongo.
Gulu lina la anthu omwe adakalowa nawo gulu lowukira laku Iraq adagwida ndi apolisi pachipikitcheni chomwe iwo adapanga kwa anthu olowa mdziko la Malasyia. Apolisi adalengeza kuti kagulu kameneka kamagwiritsa ntchito mankhwala ozunguza bongo komanso ndi anthu omwe alibe zochita mmoyo wawo komanso oluza muzochita.
Wamkulu wa apolisi adanena kuti anthu amenewa ndi opanga ntchito zoipa choncho pofuna kuti mwina azifewetsere zoipa zawo adaganiza zokalowa nawo mugululi ndicholinga choti awoneke kuti agwirako ntchito yabwino pofera munjira imeneyi.
Komabe angakhale anthu amenewa adakalowa mugululi, boma la dzikoli lidayesetsa kufotokozera anthu zakuipa kwa gulu la ISIL lomwe likugwiritsa ntchito dzina lachisilamu molakwika pomapanga zofuna zamiyoyo yawo ndikumanamizira chisilamu.
Iwo amanamizidwa kuti kufera kumeneko ndi Jihad komanso afera njira yabwino zomwe ndibodza lalikulu.
Koma zoona zake ndi zoti anthuwa ndiomwe alibe zochita komanso amamva kulemera ndizoipa zomwe akhala akuchita mapeto ake amaganiza kuti ndibwino akalowe nawo gululi.

Kuwonjezera ganizogrey Malesyians ena agwida ndi mankhwala ozunguza ubongo.
zikhale zatsopano


sharethis Malesyians ena agwida ndi mankhwala ozunguza ubongo.

Kutumiza funso

ایمیل شما منتشر نمی شود.
Malo okakamizidwa kudzadzitsamo akudziwika ndi chizindikiro ichi * .

*


× 1 = دو

Kulumikizana ndi ife | RSS |Zolinga za Site

Ufulu onse wa Site yofalitsa uthenga ya Islam 14 ndi otetezedwa ndipo zikuloledwa kugwiritsa ntchito zinthuzi potchula komwe zachokera.