Zowonedwa ndi ambiri

Chithandizo kwa ife

Pakistan idzudzula America


Pakistan idzudzula America

( 0 Votes ) 

Pakistan idzudzula America

grey Pakistan idzudzula America
 
Dziko la Pakistan ladzudzula dziko la America chifukwa cha report lomwe dzikoli lapereka.
Nkhani ikuti dziko la Pakistan lidadzudzula kazembe wa dziko la America chifukwa cha report lomwe kazembeyu adapereka lokhudzana ndi nkhani yoti dziko la Pakistan likukhudzana ndi nkhani yothandiza gulu lina lowukira mdzikomo.
Mduna yazachitetezo mdziko la Pakistan lidanena kuti zomwe gulu lina lapanga ku Afghanistan kazembeyu akulinena dziko la Pakistan kuti lidatengapo gawo pankhaniyi.
Dziko la Pakistan poyankhapo pankhani yopanda umboniyi lidalemba kalata kwa ofesi wa kazembeyu yomwe idaperekedwa ndi unduna wazachitetezo ndi Mr. Sartaj Aziz.
Kalata yomwe kazembeyu adalemba kwa unduna wa zachitetezo wa dziko la Pakistan yomwe imakwana masamba okwana zana limodzi akulu akulu mudalinso chidzudzulo choti dziko la Pakistan mudali magulu owukira mudziko la Afghanistan komanso amalimbana ndi Kabul  komanso NewDelhi kuchokera mkati ma Pakistan.
Koma dziko la Pakistan lakana nkhaniyi ponena kuti ndiyabodza komanso yopanda umboni.

Kuwonjezera ganizogrey Pakistan idzudzula America
zikhale zatsopano


sharethis Pakistan idzudzula America

Kutumiza funso

ایمیل شما منتشر نمی شود.
Malo okakamizidwa kudzadzitsamo akudziwika ndi chizindikiro ichi * .

*


یک × = 4

Kulumikizana ndi ife | RSS |Zolinga za Site

Ufulu onse wa Site yofalitsa uthenga ya Islam 14 ndi otetezedwa ndipo zikuloledwa kugwiritsa ntchito zinthuzi potchula komwe zachokera.