Zowonedwa ndi ambiri

Chithandizo kwa ife

Iran: ISIL ndiya Mossad


Iran: ISIL ndiya Mossad

( 0 Votes ) 

Iran: ISIL ndiya Mossad

grey Iran: ISIL ndiya Mossad
 
Wachiwiri kwa nduna yowona nkhani zakunja a Hossain Amir Abdullahian adadzudzula maiko akuzambwe chifukwa chothandiza gulu la ISIL. Iye mukulankhula kwake adati gulu la ISIL ndi akazitape adziko la Israel.
Iye adati ISIL ndi gulu la Mossad  lomwe adalikhazikitsa ndicholinga chofuna kuipitsa dzina la chisilamu.
Iwo pofuna kubweretsa mpungwe mpungwe mmaiko ambiri monga Syria, Iraq ndi ena akugwiritsa ntchito gululi.
Chomvetsa chisoni ndichoti iwowa akugwiritsa ntchito gululi poseweretsa chitetezo cha mmaiko ambiri.
Iye adadzudzulanso dziko la America pokhazikitsa gulu lofuna kulimbana ndi ISIL zomwe zapereka mphamvu kugululi.

Kuwonjezera ganizogrey Iran: ISIL ndiya Mossad
zikhale zatsopano


sharethis Iran: ISIL ndiya Mossad

Kutumiza funso

ایمیل شما منتشر نمی شود.
Malo okakamizidwa kudzadzitsamo akudziwika ndi chizindikiro ichi * .

*


− 1 = دو

Kulumikizana ndi ife | RSS |Zolinga za Site

Ufulu onse wa Site yofalitsa uthenga ya Islam 14 ndi otetezedwa ndipo zikuloledwa kugwiritsa ntchito zinthuzi potchula komwe zachokera.