Zowonedwa ndi ambiri

Chithandizo kwa ife

Chiwahhabi 5


Chiwahhabi 5

( 0 Votes ) 

Mudzina la Mulungu mwini chifundo ndichisoni chakuya.
Kodi  Al Yahud Wahabi ndi Takfir idapangidwa bwanji?
Kugwiritsa ntchito mfundo zamphamvu za Chisilamu
pofuna kuchifafaniza.
1- Chikhalidwe chabwino ndi Taqwa.
2- Kuletsedwa kwa zinthu zabwino monga chiwerewere, katapila, kuba, nyama yankhumba ndi zina).
3- Kupezeka kwa anthu ophunzira mu Chisilamu.
4- Kutsatira atsogoleri awo monga Mtumiki ndi atsogoleri ena.
5- Jihad.
6- Kuchitenga Chisilamu kukhala chipembedzo chapamwamba(Chikhulupiriro cha Msilamu wina aliyense).
7- Asilamu amadana ndikumangidwa kwa matchalitchi mmadera awo.
8- Kutulutsidwa kwa Ayuda kuchokera mmadera olemekezeka monga Makkah ndi Madinah (Mukutero sangathe kupanga ukazitape).
9- Asilamu ndi olimba popanga zolamulidwa zawo monga mapemphero kasanu patsiku, kusala, kupereka chaulere, kupita ku hajji ndi zina.
10- Chisilamu chimalamulira kupereka chaulere monga zakat ndi khumus zomwe zimabweretsa chuma kwa Asilamu.
11- Chisilamu chimalamulira hijab zomwe mapeto ake zimachepetsa chiwerewere pa society.
12- Chisilamu chimalimbikitsa ukwati ndikuphunzitsa ana chipembedzo chawo.
13- Chisilamu chimalimbikitsa kukhalirana limodzi ndikupanga zinthu limodzi:
Mulungu akuti:
﴿یا أَیُّهَا الَّذِینَ آمَنُوا لا یَسْخَرْ قَوْمٌ مِنْ قَوْمٍ عَسى‏ أَنْ یَکُونُوا خَیْراً مِنْهُمْ وَ لا نِساءٌ مِنْ نِساءٍ عَسى‏ أَنْ یَکُنَّ خَیْراً مِنْهُنَ﴾ (الحجرات:۱۱)‏
﴿وَ أَطِیعُوا اللَّهَ وَ رَسُولَهُ وَ لا تَنازَعُوا فَتَفْشَلُوا وَ تَذْهَبَ رِیحُکُمْ وَ اصْبِرُوا إِنَّ اللَّهَ مَعَ الصَّابِرِین﴾ (الانفال:۴۶)
۱۴- Chisilamu chimalimbikitsa zakulamulira zabwino ndikuletsa zoipa
15- Kukhala ndichikhulupiriro pazakulipidwa pambuyo popanga zabwino padziko pompano kapena tsiku lomaliza.
16- Chikhulupiriro pa swadaqatul Jariyah ( kukumba chitsime, kudzala mtengo, kuphunzitsa mwana za Mulungu…).

Kuwonjezera ganizogrey Chiwahhabi 5
zikhale zatsopano


sharethis Chiwahhabi 5

Kutumiza funso

ایمیل شما منتشر نمی شود.
Malo okakamizidwa kudzadzitsamo akudziwika ndi chizindikiro ichi * .

*


× 5 = پنج

Kulumikizana ndi ife | RSS |Zolinga za Site

Ufulu onse wa Site yofalitsa uthenga ya Islam 14 ndi otetezedwa ndipo zikuloledwa kugwiritsa ntchito zinthuzi potchula komwe zachokera.