Zowonedwa ndi ambiri

Chithandizo kwa ife

phulitsidwa kwa Nzikiti mu nzinda wa Sa’adah


phulitsidwa kwa Nzikiti mu nzinda wa Sa’adah

( 0 Votes ) 

Kuphulitsidwa kwa Nzikiti mu nzinda wa Sa’adah

grey phulitsidwa kwa Nzikiti mu nzinda wa Saadah
 
Dziko la Saud Arabia popitiliza chiwembu chomwe akuchita ku Yemen aphulitsa nzikiti omwe uli munzinda wa Sa’adah.
Olengeza nkhani anena kuti Saud Arabia idali ndi chilingaliro chophulitsa nzikitiwu omwe uli mdera la Sa’adah munziko la Yemen.
Angakhale kuti mweziwu ndiwa Ramadhan ndiponso wafika pakati komabe Saud Arabia sidasiye kuchita nkhondo mdziko la Yemen.
Press tv yanena kuti Saud Arabia yaphulitsa nzikiti omwe uli mdera la Sa’adah ndikubweretsa chiopsezo kwa anthu.
Angakhale kuti tv imeneyi sidanene mwatsatane tsatane koma kuti uku sikuyamba kuti Saud Arabia iphulitse malo olemekezeka ngati amenewa omwe ndi nzikiti mudziko la Yemen.

Kuwonjezera ganizogrey phulitsidwa kwa Nzikiti mu nzinda wa Saadah
zikhale zatsopano


sharethis phulitsidwa kwa Nzikiti mu nzinda wa Saadah

Kutumiza funso

ایمیل شما منتشر نمی شود.
Malo okakamizidwa kudzadzitsamo akudziwika ndi chizindikiro ichi * .

*


نُه + = 18

Kulumikizana ndi ife | RSS |Zolinga za Site

Ufulu onse wa Site yofalitsa uthenga ya Islam 14 ndi otetezedwa ndipo zikuloledwa kugwiritsa ntchito zinthuzi potchula komwe zachokera.