Zowonedwa ndi ambiri

Chithandizo kwa ife

Kuphulitsa kwa Ansarullah malo ena a asilikali a Saud Arabia


Kuphulitsa kwa Ansarullah malo ena a asilikali a Saud Arabia

( 0 Votes ) 

Kuphulitsa kwa Ansarullah malo ena a asilikali a Saud Arabia

 
Onena nkhani akuti Ansarullah poyankha chiwembu chomwe Saud Arabia idachita pophulitsa malo ena lachisanu lapita komwe kudasiya anthu okwana 16 ataphedwa aphulitsa malo ena omwe achita malire ndi Saud Arabia monga Najran ndi Jozon.
Mukuphulitsa kumeneku asilikali ambiri a Saud Arabia aphedwa.
Nkhani ikuti Ansarullah aaphulitsanso malo owulukira ndege a Jozon komwe asikali enanso aphedwa.
Iwo adatumiza zida zokwana 13 za Rockets zomwe zidakaononga malo okhala asilikali a dziko la Saud Arabia.
Apa mpamene Europe, America akufuna kuti agwirizane zosiya nkhondo.

Kuwonjezera ganizogrey Kuphulitsa kwa Ansarullah malo ena a asilikali a Saud Arabia
zikhale zatsopano


sharethis Kuphulitsa kwa Ansarullah malo ena a asilikali a Saud Arabia

Kutumiza funso

ایمیل شما منتشر نمی شود.
Malo okakamizidwa kudzadzitsamo akudziwika ndi chizindikiro ichi * .

*


هفت + 3 =

Kulumikizana ndi ife | RSS |Zolinga za Site

Ufulu onse wa Site yofalitsa uthenga ya Islam 14 ndi otetezedwa ndipo zikuloledwa kugwiritsa ntchito zinthuzi potchula komwe zachokera.