Zowonedwa ndi ambiri

Chithandizo kwa ife

Tsiku la Qudus


Tsiku la Qudus

( 0 Votes ) 

Tsiku la Qudus

 
Tsiku la Qudus nditsiku lomwe asilamu amakuwa posonyeza kuipidwa ndi mchitidwe opha ana ku Gaza ndi Yemen.
Gulu lankhondo la dziko la Iran laitana asilamu onse mudzikomo kuti akakhale nawo pamwambo wachionetsero pozudzula anthu ankhanza omwe akupha ana ku Gaza ndi Yemen. Iwo adati tsikuli ndi lomwe asilamu amaonetsa umodzi wawo pokuwa za ufulu wa ana ndikhanza zomwe anthu oipa akuchita popha anawa mmaiko awiriwa.
Olemba nkhani anena kuti zomwe maiko ena akuchita popha ana ndi nkhalamba mmawikowa ndi zoipa kwambiri ndipo zikusonyeza kuipa mitima kwawo.
Asilamu adziko la Iran pofuna kusonyeza kukwiya kwawo pankhaniyi akuyenerezeka kubwera kudzakhala nawo pamwambowu.

Kuwonjezera ganizogrey Tsiku la Qudus
zikhale zatsopano


sharethis Tsiku la Qudus

Kutumiza funso

ایمیل شما منتشر نمی شود.
Malo okakamizidwa kudzadzitsamo akudziwika ndi chizindikiro ichi * .

*


سه − 2 =

Kulumikizana ndi ife | RSS |Zolinga za Site

Ufulu onse wa Site yofalitsa uthenga ya Islam 14 ndi otetezedwa ndipo zikuloledwa kugwiritsa ntchito zinthuzi potchula komwe zachokera.