Zowonedwa ndi ambiri

Chithandizo kwa ife

Ana ambiri ndi omwe akuphedwa.


Ana ambiri ndi omwe akuphedwa.

( 0 Votes ) 

Ana ambiri ndi omwe akuphedwa.

grey Ana ambiri ndi omwe akuphedwa.
 
Nkhondo yomwe ikuchitika ku Gaza tikawerengetsera chiwerengero cha ophedwa tipeza kuti ana ndi amene akuphedwa kwambiri kusiyana ndi akuluakulu.
Olemba nkhani akuti nkhondo yamasiku 51 yaku Gaza yasiya nambala yayikulu ya ana ophedwa.
Bungwe lofalitsa nkhani la Tasnim lidalemba nkhaniyi potengera kwa mtolankhani waku France kuti madokotala kuchipatala alengezetsa zoti kwa anthu omwe akuwathandiza kuchipatala chawo ndi ana ambiri omwe akubweretsedwa kwa iwo poyerekeza ndi akuluakulu zomwe zikusonyeza kuti omwe aphedwa kwambiri mu masiku 51 amenewa ndi ana.
Mu report lomwe lanenedwa nkhani ikuti nkhondo yomwe idayamba pa 8 July mpaka idatenga masiku okwana 51 anthu okwana 2200 aphedwa ku Palestine ndipo kuchokera munambala imeneyi nambala yayikulu ndiya ana.
 

Kuwonjezera ganizogrey Ana ambiri ndi omwe akuphedwa.
zikhale zatsopano


sharethis Ana ambiri ndi omwe akuphedwa.

Kutumiza funso

ایمیل شما منتشر نمی شود.
Malo okakamizidwa kudzadzitsamo akudziwika ndi chizindikiro ichi * .

*


× 9 = شصت سه

Kulumikizana ndi ife | RSS |Zolinga za Site

Ufulu onse wa Site yofalitsa uthenga ya Islam 14 ndi otetezedwa ndipo zikuloledwa kugwiritsa ntchito zinthuzi potchula komwe zachokera.