Zowonedwa ndi ambiri

Chithandizo kwa ife

Kumasula kusala ndichakudya cha poison


Kumasula kusala ndichakudya cha poison

( 0 Votes ) 

 
Kumasula kusala ndichakudya cha poison
 

grey Kumasula kusala ndichakudya cha poison
Nkhani ikuti anthu ambiri agulu la Isil (Daish) amwalira ndichakudya chothira poison chomwe adamasulira nacho kusala kwawo.
Gululi limalanga munthu yemwe angakhale ndichikaikiro paza kumasula kusala kwake popereka 80 dollars ndiponso ozionetsera nthawi yomasula pomunyonga.
Newspepala ya Al sumariyyah yalemba kuti anthu okwana 145 agululi adapatsidwa chakudya chothiridwa poison ndipo okwana 45 adamwalira.
Izi zikuchitika pambuyo poti anthuwa adapha anthu ambiri adera la Musil ndipo anthu ena pofuna kubwezera ndiye adawathirira chakudya poison.
Kwachaka tsopano Isil ikulamulira dera la Musil ndi madera ena ozungulira ilo, iwo akhala akuvutitsa anthu aderali ndipo yense okaikira zakumasula kwake amamulipilitsa ndalama zokwana 80 dollars ndipo omasula mozionetsera amalamulidwa kuti anyongedwe.
Gululi lakhala likukakamiza anthu amuderali kuti ayenera kutsatira iwo.
 

Kuwonjezera ganizogrey Kumasula kusala ndichakudya cha poison
zikhale zatsopano


sharethis Kumasula kusala ndichakudya cha poison

Kutumiza funso

ایمیل شما منتشر نمی شود.
Malo okakamizidwa kudzadzitsamo akudziwika ndi chizindikiro ichi * .

*


− 1 = دو

Kulumikizana ndi ife | RSS |Zolinga za Site

Ufulu onse wa Site yofalitsa uthenga ya Islam 14 ndi otetezedwa ndipo zikuloledwa kugwiritsa ntchito zinthuzi potchula komwe zachokera.