Zowonedwa ndi ambiri

Chithandizo kwa ife

Shirazi ithandiza anthu aku Gaza ndi Yemen


Shirazi ithandiza anthu aku Gaza ndi Yemen

( 0 Votes ) 

Shirazi ithandiza anthu aku Gaza ndi Yemen


 
Anthu anzinda wa Shirazi mdziko la Iran adathandiza anthu anzinda wa Gaza ndi Yemen.
Wamkulu wa committee ya chithandizo chotchedwa Imam Khumeini adati anthu amunzinda wa Shirazi adathandiza asilamu oponderezedwa adera la Gaza komanso dziko la Yemen ndi ndalama zokwana 312 million Rial.
Murat Rasuli pofuna kuyamika anthu anzindawu adanena kuti anthu aderali adaonetsa chinthu chabwino kwambiri mu mwezi uno wa Ramadhan chomwe asilamu ena ayenera kutengera phunziro posonkhaniza ndalama zambiri ngati zimenezi ndizina posakhala ndalama pofuna kuthandiza anthu omwe akuvutika ku Gaza ndi Yemen.
  Anthuwa adasonkhanitsa ndalama zimenezi pamene adali pachionetsero chadziko lonse lapansi cha tsiku la Qudus ndipo ndalama zokwana 146 million Rial zothandizira anthu aku Palestine (Gaza) pomwe 166 million Rial zothandizira anthu aku Yemen.
Iye adawonjezera kuti ndalama zimenezi zitumizidwa mmaiko oyenera mofulumira.

Kuwonjezera ganizogrey Shirazi ithandiza anthu aku Gaza ndi Yemen
zikhale zatsopano


sharethis Shirazi ithandiza anthu aku Gaza ndi Yemen

Kutumiza funso

ایمیل شما منتشر نمی شود.
Malo okakamizidwa kudzadzitsamo akudziwika ndi chizindikiro ichi * .

*


3 + = ده

Kulumikizana ndi ife | RSS |Zolinga za Site

Ufulu onse wa Site yofalitsa uthenga ya Islam 14 ndi otetezedwa ndipo zikuloledwa kugwiritsa ntchito zinthuzi potchula komwe zachokera.