Zowonedwa ndi ambiri

Chithandizo kwa ife

Chiwahhabi 6


Chiwahhabi 6

( 0 Votes ) 

Mudzina la Mulungu mwini chifundo ndichisoni chosatha.
Zoopsa za kupezeka kwa Chiwahabi
Zichitochito za anthu ofuna kulamulira dziko lapansi
Pofuna kufafaniza Chisilamu
Kodi Chisilamu  tichifafanize bwanji?
Zofowoka za Asilamu ndi ziti?
Henfry  yemwe ndi Kazitape wa America adali kunena kuti: Nthawi yomwe ndidali malo amodzi mwa malo omwe ndimatumizidwa kukapanga ukazitape, tsiku lina adandilowetsa muchinyumba chomwe chidali ndi zipinda zambiri, ndiye nzipinda mmenemu mudali mashaikh osiyana siyana omwe amaimira ma shaikh mmadera ndi mathahab osiyana siyana.Ndidafunsa kuti kodi anthu amenewa ndiofunikira bwanji? Adandiyankha kuti mashaikh amenewa ndioti maphunziro onse omwe mashaikh amadera amenewo komanso mathahab amenewo alinawo iwowanso alinawo.Kuchokera apa timakwanitsa kupanga ntchito zathu mosavutikira. Ndidayesa kumufunsa mmodzi wawo zankhani ina yomwe ndimaidziwa bwino koma adandiyankha chimodzi modzi momga momwe mashaikh eni ake chisilamu amadziwila.
Kenako adandionetsa bukhu ndikundiuza kuti bukhu ili ndizotsatira zakafukufuku amene tachita paza Chisilamu komanso zokambirana zomwe  zachitika pakati pathu ndi mashaikh achisilamu. Mmenemu muli mfundo zofowoka zachisilamu komanso zamphamvu za Chisilamu ndiponso muli njira zolimbana ndi zimenezi.(Monga kugwetsa ulamuliro wa Uthmani omwe udali wamphamvu munthawi imeneyo omwe udakhala kwazaka 600), apa ndipomwe ndidatsimikiza kuti ulamuliro umenewu udzagwetsedwa komanso Chisilamu chidzathetsedwa.
Zofooka za Chisilamu:
1- Kusiyana maganizo komwe kulipo pakati pa asilamu( mathahab, Mutazir ndi Ashairi, shia ndi sunni…).
۲- Umbuli wa asilamu ena pachipembedzo chawo.
3- Kutalikirana ndi dziko.
4- Kupezeka kwa olamula opondereza kapati pa Asilamu.
5- Kusokoneza chitetezo cha Asilamu.
6- Kuchepetsa chitukuko cha ulimi pakati pa Asilamu (Kenako ndiye amabwera ndikumathandiza ngati anthu abwino).
7- Kayendetsedwe kazinthu kosokonekera (monga ziphuphu, kuphangira pothandiza abale posiya anthu ena ndi zina).
8- Kufooka pachuma.
9- Kusakhala ndi gulu lankhondo lamphamvu.
10- Umve kwambiri kwake mmisika yawo.

Kuwonjezera ganizogrey Chiwahhabi 6
zikhale zatsopano


sharethis Chiwahhabi 6

Kutumiza funso

ایمیل شما منتشر نمی شود.
Malo okakamizidwa kudzadzitsamo akudziwika ndi chizindikiro ichi * .

*


9 − = سه

Kulumikizana ndi ife | RSS |Zolinga za Site

Ufulu onse wa Site yofalitsa uthenga ya Islam 14 ndi otetezedwa ndipo zikuloledwa kugwiritsa ntchito zinthuzi potchula komwe zachokera.